2 Samueli 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Manja ako sanali omangidwa,+Ndipo mapazi ako sanaikidwe m’matangadza amkuwa.+Wagwa ngati munthu wogwa pamaso pa anthu osalungama.”+Pamenepo anthu onse anamuliranso.+ 2 Samueli 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+
34 Manja ako sanali omangidwa,+Ndipo mapazi ako sanaikidwe m’matangadza amkuwa.+Wagwa ngati munthu wogwa pamaso pa anthu osalungama.”+Pamenepo anthu onse anamuliranso.+
3 Zitatero, Davide anatuma nthumwi kukafufuza za mkaziyo.+ Ndiyeno munthu wina ananena kuti: “Kodi ameneyu si Bati-seba+ mwana wa Eliyamu,*+ mkazi wa Uriya+ Mhiti?”+