Genesis 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usakhale wopambana, chifukwa ndi khalidwe lako lotayirira ngati madzi osefukira,+ unakwera pogona bambo ako.+ Unaipitsa bedi langa pa nthawiyo.+ Anagonapo ndithu ameneyu!
4 Usakhale wopambana, chifukwa ndi khalidwe lako lotayirira ngati madzi osefukira,+ unakwera pogona bambo ako.+ Unaipitsa bedi langa pa nthawiyo.+ Anagonapo ndithu ameneyu!