Salimo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye wafukula dzenje, walikumbadi.+Koma adzagwera m’dzenje lokumba yekha.+ Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]