Salimo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+Chifukwa iwo akupandukirani.+ Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+
10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+Chifukwa iwo akupandukirani.+
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipa kumanda.+Ndipo anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso anthu achinyengo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+Koma ine ndidzakhulupirira inu.+