2 Samueli 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Barizilai anali wokalamba kwambiri pakuti anali ndi zaka 80.+ Pamene mfumu inali kukhala ku Mahanaimu,+ Barizilai anali kuipatsa chakudya pakuti iye anali munthu wolemera kwambiri.+ 1 Mafumu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ana a Barizilai+ Mgiliyadi uwasonyeze kukoma mtima kosatha. Azikhala pakati pa anthu odyera nawe limodzi patebulo,+ chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinali kuthawa m’bale wako Abisalomu.+
32 Barizilai anali wokalamba kwambiri pakuti anali ndi zaka 80.+ Pamene mfumu inali kukhala ku Mahanaimu,+ Barizilai anali kuipatsa chakudya pakuti iye anali munthu wolemera kwambiri.+
7 “Ana a Barizilai+ Mgiliyadi uwasonyeze kukoma mtima kosatha. Azikhala pakati pa anthu odyera nawe limodzi patebulo,+ chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinali kuthawa m’bale wako Abisalomu.+