1 Mafumu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo ukayenda m’njira zanga mwa kusunga malangizo ndi malamulo anga+ monga momwe Davide bambo ako anayendera,+ ndidzatalikitsanso masiku ako.”+ 1 Mafumu 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+
14 Ndipo ukayenda m’njira zanga mwa kusunga malangizo ndi malamulo anga+ monga momwe Davide bambo ako anayendera,+ ndidzatalikitsanso masiku ako.”+
5 Anatero popeza Davide anachita zoyenera pamaso pa Yehova, ndipo sanapatuke pa chilichonse chimene Mulungu anamulamula masiku onse a moyo wake,+ kupatulapo pa nkhani ya Uriya Mhiti.+