Deuteronomo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale ku Horebe, inu munaputa mkwiyo wa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo analitu kumupandukira kawirikawiri m’chipululu,+Anali kumukhumudwitsa m’chipululumo!+
8 Ngakhale ku Horebe, inu munaputa mkwiyo wa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+