41 Ndiyeno uzipereka mwana wa nkhosa wachiwiri madzulo kuli kachisisira. Um’pereke pamodzi ndi nsembe yambewu+ yofanana ndi ya m’mawa komanso ndi nsembe yake yachakumwa. Uzipereke monga fungo lokhazika mtima pansi, nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.