Mika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+ Mika 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.
2 “Tsoka kwa anthu amene amati akagona pabedi, amakonza chiwembu ndiponso kuganiza mmene angachitire zoipa.+ M’mawa kukangocha, iwo amazichitadi+ chifukwa chakuti ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+
3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita bwino kwambiri.+ Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso, ndipo woweruza amalandira chiphuphu poweruza.+ Munthu wotchuka amangolankhula zolakalaka za mtima wake+ ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.