11 Pamenepo Yehosafati anati:+ “Kodi kuno kulibe mneneri wa Yehova?+ Ngati alipo tiyeni tifunsire kwa Yehova kudzera mwa iye.”+ Ndiyeno mmodzi mwa atumiki a mfumu ya Isiraeli anayankha kuti: “Kuli Elisa+ mwana wa Safati, amene anali kuthirira Eliya madzi osamba m’manja.”+