2 Samueli 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atanena mawu amenewa, Yowabu anachoka pamaso pa Davide ndipo anatumiza mithenga kuti itsatire Abineri. Mithengayo inabweza Abineri+ pachitsime cha Sira, koma Davide sanadziwe kena kalikonse.
26 Atanena mawu amenewa, Yowabu anachoka pamaso pa Davide ndipo anatumiza mithenga kuti itsatire Abineri. Mithengayo inabweza Abineri+ pachitsime cha Sira, koma Davide sanadziwe kena kalikonse.