2 Samueli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi. 1 Mbiri 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yonatani,+ mwana wa m’bale wake wa Davide, anali phungu wanzeru+ komanso mlembi. Yehiela mwana wa Hakimoni+ ndiye anali kuyang’anira ana a mfumu.+
17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi.
32 Yonatani,+ mwana wa m’bale wake wa Davide, anali phungu wanzeru+ komanso mlembi. Yehiela mwana wa Hakimoni+ ndiye anali kuyang’anira ana a mfumu.+