1 Mafumu 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu Solomo inaitana anthu ogwira ntchito yokakamiza+ kuti adzamange nyumba ya Yehova,+ nyumba yake, Chimulu cha Dothi,*+ khoma+ lozungulira Yerusalemu, ndiponso mizinda ya Hazori,+ Megido,+ ndi Gezeri.+
15 Mfumu Solomo inaitana anthu ogwira ntchito yokakamiza+ kuti adzamange nyumba ya Yehova,+ nyumba yake, Chimulu cha Dothi,*+ khoma+ lozungulira Yerusalemu, ndiponso mizinda ya Hazori,+ Megido,+ ndi Gezeri.+