Yoswa 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 koma mutengenso dera lamapiri.+ Poti ndi lankhalango, mudulemo mitengo ndipo gawo lanu likathere kumeneko. Mupitikitse Akanani, ngakhale kuti ndi amphamvu ndipo ali ndi magaleta ankhondo okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.”+
18 koma mutengenso dera lamapiri.+ Poti ndi lankhalango, mudulemo mitengo ndipo gawo lanu likathere kumeneko. Mupitikitse Akanani, ngakhale kuti ndi amphamvu ndipo ali ndi magaleta ankhondo okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.”+