Numeri 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yairi mwana wa Manase ananyamuka ulendo wokalanda midzi yawo ing’onoing’ono. Midzi imeneyi anaitcha kuti Havoti-yairi.+ Deuteronomo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri+ ndi a Amaakati,+ ndipo midzi ya ku Basana imeneyo anaitcha dzina la iye mwini lakuti, Havoti-yairi*+ kufikira lero.
41 Yairi mwana wa Manase ananyamuka ulendo wokalanda midzi yawo ing’onoing’ono. Midzi imeneyi anaitcha kuti Havoti-yairi.+
14 “Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri+ ndi a Amaakati,+ ndipo midzi ya ku Basana imeneyo anaitcha dzina la iye mwini lakuti, Havoti-yairi*+ kufikira lero.