1 Samueli 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Davide anayankha Sauli kuti: “Ndine yani ine, ndipo abale anga, anthu a m’banja la bambo anga ndani mu Isiraeli monse muno kuti ndikhale mkamwini wa mfumu?”+
18 Koma Davide anayankha Sauli kuti: “Ndine yani ine, ndipo abale anga, anthu a m’banja la bambo anga ndani mu Isiraeli monse muno kuti ndikhale mkamwini wa mfumu?”+