16 Koma panalibe njira yodziwira kulemera kwa mkuwa wa zipilala ziwiri zija, chosungiramo madzi chimodzi chija, ndi zotengera zokhala ndi mawilo zimene Solomo anapangira nyumba ya Yehova. Panalibe njira yodziwira kulemera kwa mkuwa wa ziwiya zonsezi.+