1 Mafumu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Hiramu+ atangomva mawu a Solomo, anasangalala kwambiri ndipo ananena kuti: “Yehova atamandike+ lero, popeza wapereka kwa Davide mwana wanzeru+ woti alamulire anthu ochulukawa.”+ Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+
7 Hiramu+ atangomva mawu a Solomo, anasangalala kwambiri ndipo ananena kuti: “Yehova atamandike+ lero, popeza wapereka kwa Davide mwana wanzeru+ woti alamulire anthu ochulukawa.”+