2 Mbiri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anayenda m’njira za mafumu a Isiraeli,+ ndipo anafika mpaka popangira Abaala+ zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula.+
2 Koma anayenda m’njira za mafumu a Isiraeli,+ ndipo anafika mpaka popangira Abaala+ zifaniziro zopangidwa ndi zitsulo zosungunula.+