Mateyu 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa, ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina, ndipo musalowe mumzinda wa Asamariya.+
5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa, ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina, ndipo musalowe mumzinda wa Asamariya.+