Deuteronomo 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mose atangomaliza kulemba mawu onse a chilamulo ichi m’buku,+ Deuteronomo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Tengani buku ili la chilamulo,+ muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, kuti likhale mboni ya Mulungu yokutsutsani.+ 2 Mbiri 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamene anali kutulutsa ndalama+ zimene zinali kubwera kunyumba ya Yehova, wansembe Hilikiya+ anapeza buku+ la chilamulo cha Yehova+ loperekedwa ndi dzanja la Mose.+
26 “Tengani buku ili la chilamulo,+ muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, kuti likhale mboni ya Mulungu yokutsutsani.+
14 Pamene anali kutulutsa ndalama+ zimene zinali kubwera kunyumba ya Yehova, wansembe Hilikiya+ anapeza buku+ la chilamulo cha Yehova+ loperekedwa ndi dzanja la Mose.+