50 mabeseni, zozimitsira nyale,+ mbale zolowa,+ makapu,+ ndi zopalira moto.+ Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino. Anapanganso molowa miyendo ya zitseko+ za chipinda chamkati, kutanthauza Chipinda Choyera Koposa, ndiponso molowa miyendo ya zitseko+ za nyumbayo.+ Zonsezi zinali zagolide.