1 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno anakumbatira mwanayo+ katatu ali pabedipo n’kufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga, chonde chititsani kuti moyo+ wa mwanayu ubwerere mwa iye.” Machitidwe 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Paulo anatsika pansi, ndipo anadziponya pa iye+ ndi kumukumbatira. Kenako ananena kuti: “Khalani chete, pakuti ali moyo tsopano.”+
21 Ndiyeno anakumbatira mwanayo+ katatu ali pabedipo n’kufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga, chonde chititsani kuti moyo+ wa mwanayu ubwerere mwa iye.”
10 Koma Paulo anatsika pansi, ndipo anadziponya pa iye+ ndi kumukumbatira. Kenako ananena kuti: “Khalani chete, pakuti ali moyo tsopano.”+