9 Zitatero, ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase, anachoka ku Silo kumene kunali ana ena a Isiraeli m’dziko la Kanani. Anapita ku Giliyadi,+ dziko lawo limene anapatsidwa ndi Mose molamulidwa ndi Yehova, ndiponso limene anakhazikikamo.+