Genesis 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Sara anakhala akuona mwana amene Hagara Mwiguputo+ anaberekera Abulahamu akuseka Isaki.+ 2 Mbiri 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera. Luka 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.” 1 Atesalonika 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho munthu wonyalanyaza+ chiphunzitso chimenechi sakunyalanyaza munthu, koma Mulungu+ amene amaika mzimu wake woyera+ mwa inu.
16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera.
16 “Amene akukumverani,+ akumveranso ine. Ndipo amene akunyalanyaza+ inu akunyalanyazanso ine. Ndipotu amene akunyalanyaza ine akunyalanyazanso amene anandituma.”
8 Choncho munthu wonyalanyaza+ chiphunzitso chimenechi sakunyalanyaza munthu, koma Mulungu+ amene amaika mzimu wake woyera+ mwa inu.