1 Mafumu 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo nawonso anapitiriza kudzimangira malo okwezeka,+ zipilala zopatulika,+ ndi mizati yopatulika+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali,+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+ Yeremiya 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngakhale ana awo aamuna akumbukira maguwa awo ansembe ndi mizati yawo yopatulika imene ili pansi pa mtengo waukulu wamasamba ambiri obiriwira, pamwamba pa zitunda zazitali+
23 Ndipo nawonso anapitiriza kudzimangira malo okwezeka,+ zipilala zopatulika,+ ndi mizati yopatulika+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali,+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+
2 Ngakhale ana awo aamuna akumbukira maguwa awo ansembe ndi mizati yawo yopatulika imene ili pansi pa mtengo waukulu wamasamba ambiri obiriwira, pamwamba pa zitunda zazitali+