2 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo.
6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo.