-
1 Mafumu 15:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Asa ataona zimenezi anatenga siliva ndi golide yense amene anatsala pa chuma cha m’nyumba ya Yehova, ndi pa chuma cha m’nyumba ya mfumu, n’kumupereka kwa atumiki ake. Kenako Mfumu Asa inatumiza atumiki akewo kwa Beni-hadadi+ mwana wa Tabirimoni, mwana wa Hezioni, mfumu ya Siriya,+ amene anali kukhala ku Damasiko.+ Inawatuma kuti akamuuze Beni-hadadi kuti:
-