25 Thankiyo anaikhazika pang’ombe zamphongo 12.+ Ng’ombe zitatu zinayang’ana kumpoto, zitatu zinayang’ana kumadzulo, zitatu zinayang’ana kum’mwera, ndipo zitatu zinayang’ana kum’mawa. Thankiyo inali pamwamba pa ng’ombezo ndipo mbuyo zonse za ng’ombezo zinaloza pakati.+