Ekisodo 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mitengo yonyamulirayo anailowetsa m’mphete zam’mbali mwa Likasa zija kuti azinyamulira Likasalo.+ Numeri 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu,*+ n’kuyalanso nsalu yabuluu pamwamba pake. Kenako azibwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+ 2 Mbiri 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mitengo yonyamulirayo inali yaitali, moti nsonga zake zinali kuonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+
6 Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu,*+ n’kuyalanso nsalu yabuluu pamwamba pake. Kenako azibwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+
9 Koma mitengo yonyamulirayo inali yaitali, moti nsonga zake zinali kuonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+