1 Mbiri 6:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 M’bale wake Asafu+ anali kutumikira mbali ya kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya,+ Berekiya anali mwana wa Simeya, 1 Mbiri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe,+ Netaniya, ndi Asarela.+ Ana ake amenewa anali kuyang’aniridwa ndi Asafuyo,+ amenenso anali mneneri wa mfumu. Salimo 83:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nyimbo ndi Salimo la Asafu.+
39 M’bale wake Asafu+ anali kutumikira mbali ya kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya,+ Berekiya anali mwana wa Simeya,
2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe,+ Netaniya, ndi Asarela.+ Ana ake amenewa anali kuyang’aniridwa ndi Asafuyo,+ amenenso anali mneneri wa mfumu.