Genesis 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+ Genesis 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo.
20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+
6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo.