Yoswa 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ku Sefela+ kunali Esitaoli,+ Zora,+ Asina, Oweruza 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako mzimu wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa iye ku Mahane-dani+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+ 1 Mbiri 2:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Mabanja a Kiriyati-yearimu anali Aitiri,+ Aputi, Asumati, ndi Amisirai. Azorati+ ndi Aesitaoli+ anachokera ku mabanja amenewa.
25 Kenako mzimu wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa iye ku Mahane-dani+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+
53 Mabanja a Kiriyati-yearimu anali Aitiri,+ Aputi, Asumati, ndi Amisirai. Azorati+ ndi Aesitaoli+ anachokera ku mabanja amenewa.