Ekisodo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo ana aamuna a Uziyeli anali Misayeli, Elizafana ndi Sitiri.+ Numeri 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana a Kohati,+ malinga ndi mayina a mabanja awo, anali Amuramu, Izara,+ Heburoni ndi Uziyeli.