Yoswa 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Malire a gawo lawo anadutsa ku Helikati,+ Hali, Beteni, Akasafu,+ Yoswa 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Helikati+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Rehobu+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.
31 Helikati+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Rehobu+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.