Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Genesis 49:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Benjamini adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ M’mawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zimene wafunkha.”+ Numeri 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amenewa ndiwo anali ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,600.+
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+
27 “Benjamini adzapitiriza kukhadzula ngati mmbulu.+ M’mawa adzadya nyama imene wagwira, ndipo madzulo adzagawa zimene wafunkha.”+
41 Amenewa ndiwo anali ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 45,600.+