2 Mafumu 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Patapita nthawi, anthu ena anagwirizana zom’chitira chiwembu+ ku Yerusalemu, choncho iye anathawira ku Lakisi.+ Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko n’kukamuphera komweko.+
19 Patapita nthawi, anthu ena anagwirizana zom’chitira chiwembu+ ku Yerusalemu, choncho iye anathawira ku Lakisi.+ Koma anthuwo anatumiza anthu ena omwe anamutsatira ku Lakisiko n’kukamuphera komweko.+