1 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo. 2 Mbiri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa+ kuti Ahaziya awonongeke+ mwa kupita kwa Yehoramu. Atafika kumeneko, anatengana+ ndi Yehoramu n’kupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ yemwe Yehova anam’dzoza+ kuti aphe a m’nyumba ya Ahabu.+
15 Mfumuyo sinamvere anthuwo+ chifukwa zinthu zinatembenuka chonchi mwa kufuna kwa Yehova,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula+ kwa Yerobowamu mwana wa Nebati, kudzera mwa Ahiya+ Msilo.
7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa+ kuti Ahaziya awonongeke+ mwa kupita kwa Yehoramu. Atafika kumeneko, anatengana+ ndi Yehoramu n’kupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ yemwe Yehova anam’dzoza+ kuti aphe a m’nyumba ya Ahabu.+