-
2 Mbiri 14:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho iye anauza Ayuda kuti: “Tiyeni timange mizindayi ndi mipanda+ yoizungulira. Timangenso nsanja+ ndipo tipange makomo a zitseko ziwiriziwiri ndi mipiringidzo.+ Malo m’dzikoli akadalipo chifukwa tafunafuna Yehova Mulungu wathu.+ Tam’funafuna ndipo watipatsa mpumulo pakati pa adani athu onse otizungulira.”+ Chotero iwo anamangadi ndipo zinthu zinawayendera bwino.+
-