1 Mafumu 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 M’kupita kwa nthawi Hiramu+ anapanga mabeseni,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Kenako iye anamaliza+ ntchito yonse imene anali kugwirira Mfumu Solomo, yokhudza nyumba ya Yehova.
40 M’kupita kwa nthawi Hiramu+ anapanga mabeseni,+ mafosholo+ ndi mbale zolowa.+ Kenako iye anamaliza+ ntchito yonse imene anali kugwirira Mfumu Solomo, yokhudza nyumba ya Yehova.