Ekisodo 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anapanga ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo. Anapanga ndowa, mafosholo, mbale zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto. Ziwiya zake zonse anazipanga ndi mkuwa.+
3 Kenako anapanga ziwiya zonse zogwiritsa ntchito paguwalo. Anapanga ndowa, mafosholo, mbale zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto. Ziwiya zake zonse anazipanga ndi mkuwa.+