22 M’chaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya,+ Yehova analimbikitsa mtima+ wa Koresi mfumu ya Perisiya kuti mawu a Yehova+ kudzera mwa Yeremiya+ akwaniritsidwe. Pamenepo Koresiyo anatumiza mawu amene analengezedwa mu ufumu wake wonse. Mawuwo analembedwanso m’makalata,+ kuti: