2 Mafumu 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Koma woperekera chakudyayo anati: “Ndingagawire bwanji chakudya chimenechi anthu 100?”+ Elisa ananena kuti: “Gawira anthuwa kuti adye, pakuti Yehova wanena kuti, ‘Anthuwa adya mokwanira chakudyachi, ndipo chitsala.’”+
43 Koma woperekera chakudyayo anati: “Ndingagawire bwanji chakudya chimenechi anthu 100?”+ Elisa ananena kuti: “Gawira anthuwa kuti adye, pakuti Yehova wanena kuti, ‘Anthuwa adya mokwanira chakudyachi, ndipo chitsala.’”+