Yesaya 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani+ ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’ Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+
18 Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani+ ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’ Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+