Deuteronomo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzikumbukira njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakuyendetsani m’chipululu zaka 40 zonsezi.+ Iye anakuyendetsani m’chipululu kuti akuphunzitseni kudzichepetsa,+ kukuyesani+ pofuna kudziwa zimene zinali mumtima mwanu,+ kuti aone ngati mukanasunga malamulo ake kapena ayi. Salimo 139:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndifufuzeni, inu Mulungu, ndi kudziwa mtima wanga.+Ndisanthuleni ndi kudziwa malingaliro anga amene akundisowetsa mtendere,+
2 Muzikumbukira njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakuyendetsani m’chipululu zaka 40 zonsezi.+ Iye anakuyendetsani m’chipululu kuti akuphunzitseni kudzichepetsa,+ kukuyesani+ pofuna kudziwa zimene zinali mumtima mwanu,+ kuti aone ngati mukanasunga malamulo ake kapena ayi.
23 Ndifufuzeni, inu Mulungu, ndi kudziwa mtima wanga.+Ndisanthuleni ndi kudziwa malingaliro anga amene akundisowetsa mtendere,+