2 Mbiri 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dzanja la Mulungu woona linakhalanso ndi anthu a ku Yuda, moti anawapatsa mtima umodzi+ kuti amvere lamulo+ la mfumu ndi la akalonga pa nkhani zokhudza kutumikira Yehova.+ 2 Mbiri 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso Manase anakonza guwa lansembe la Yehova+ n’kuyamba kuperekerapo nsembe zachiyanjano+ ndi zoyamikira,+ ndipo anauza Ayuda kuti azitumikira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+
12 Dzanja la Mulungu woona linakhalanso ndi anthu a ku Yuda, moti anawapatsa mtima umodzi+ kuti amvere lamulo+ la mfumu ndi la akalonga pa nkhani zokhudza kutumikira Yehova.+
16 Komanso Manase anakonza guwa lansembe la Yehova+ n’kuyamba kuperekerapo nsembe zachiyanjano+ ndi zoyamikira,+ ndipo anauza Ayuda kuti azitumikira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+