2 Choncho mfumu inaitana Agibeoni+ ndi kulankhula nawo. (Agibeoni sanali ana a Isiraeli koma otsala mwa Aamori.+ Ana a Isiraeli analumbira kwa Aamori,+ koma Sauli anali kufuna kuwapha+ onse chifukwa chakuti iye anali kuchitira nsanje+ ana a Isiraeli ndi ana a Yuda.)