1 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+ Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ Miyambo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wodala ndi munthu amene wapeza nzeru,+ ndiponso munthu amene wapeza kuzindikira,+ Yakobo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+
9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+
5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+