-
1 Samueli 22:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pamenepo mfumu inauza asilikali othamanga+ amene anaima pamaso pake kuti: “Tembenukani ndi kupha ansembe a Yehova chifukwa ali kumbali ya Davide. Iwo anali kudziwanso kuti Davide ndi wothawa koma sanaulule kwa ine!”+ Koma atumiki a mfumuwo sanafune kutambasula manja awo kuti akanthe ansembe a Yehova.+
-