1 Mafumu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Mfumu Rehobowamu inapanga zishango zamkuwa m’malomwake, ndipo inazipereka kwa akulu a asilikali othamanga,+ omwe anali alonda a pakhomo la nyumba ya mfumu, kuti aziziyang’anira.+
27 Choncho Mfumu Rehobowamu inapanga zishango zamkuwa m’malomwake, ndipo inazipereka kwa akulu a asilikali othamanga,+ omwe anali alonda a pakhomo la nyumba ya mfumu, kuti aziziyang’anira.+